Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nchenche zakufa zinunkhitsa moipa nizioletsa mafuta onunkhira a sing'anga; comweco kupusa kwapang'ono kuipitsa iye amene achuka cifukwa ca nzeru ndi ulemu.

2. Wanzeru, mtima wace uli ku dzanja lace lamanja; koma citsiru, mtima wace kulamanzere.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 10