Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 8:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Pamene anakhazika mlengalenga ndinali pompo;Pamene analemba pazozama kwete kwete;

28. Polimbitsa Iye thambo la kumwamba,Pokula akasupe a zozama.

29. Poikira nyanja malire ace,Kuti madzi asapitirire pa lamulo lace;Polemba maziko a dziko,

Werengani mutu wathunthu Miyambi 8