Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 8:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi nzeru siitana,Luntha ndi kukweza mau ace?

2. Iima pamwamba pa mtunda,Pa mphambano za makwalala;

3. Pambali pa cipata polowera m'mudzi,Polowa anthu pa makomo ipfuula:

Werengani mutu wathunthu Miyambi 8