Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 7:25-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Mtima wako usapatukire ku njira ya mkaziyo,Usasocere m'mayendedwe ace.

26. Pakuti amagwetsa ambiri, atawalasa;Ndipo ophedwa ndi iye acurukadi.

27. Nyumba yace ndiyo njira ya kumanda,Yotsikira ku zipinda za imfa.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 7