Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 6:34-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Pakuti nsanje ndiyo ukali wa mwamuna,Ndipo sadzacitira cifundo tsiku lobwezera cilango.

35. Sadzalabadira ciombolo ciri conse,Sadzapembedzeka ngakhale ucurukitsa malipo,

Werengani mutu wathunthu Miyambi 6