Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 6:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Adzakutsogolera ulikuyenda,Ndi kukudikira uli m'tulo,Ndi kulankhula nawe utauka.

23. Pakuti malangizo ndi nyali, malamulo ndi kuunika;Ndi zidzudzulo za mwambo ndizo njira ya moyo;

24. Zikucinjiriza kwa mkazi woipa,Ndi ku lilime losyasyalika la mkazi waciwerewere.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 6