Miyambi 6:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mboni yonama yonong'ona mabodza,Ndi wopikisanitsa abale. Uwamange pamtima pako osaleka;Uwalunze pakhosi pako.