Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 6:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mwananga, ngati waperekera mnzako cikole,Ngati wapangana kulipirira mlendo,

2. Wakodwa ndi mau a m'kamwa mwako,Wagwidwa ndi mau a m'kamwa mwako.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 6