Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 4:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Tenga nzeru, tenga luntha;Usaiwale, usapatuke pa mau a m'kamwa mwanga;

6. Usasiye nzeru, ndipo Idzakusunga;Uikonde, idzakucinjiriza.

7. Nzeru ipambana, tatenga nzeru;M'kutenga kwako konseko utenge luntha.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 4