Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 31:25-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Abvala mphamvu ndi ulemu;Nangoseka nthawi ya m'tsogolo.

26. Atsegula pakamwa pace ndi nzeru,Ndipo cilangizo ca cifundo ciri pa lilime lace.

27. Ayang'anira mayendedwe a banja lace,Sadya zakudya za ulesi.

28. Anace adzanyamuka, nadzamucha wodala;Mwamuna wace namtama, nati,

Werengani mutu wathunthu Miyambi 31