Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 31:21-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Saopera banja lace cipale cofewa;Pakuti banja lace lonse libvala mlangali.

22. Adzipangira zimbwi zamaangamaanga;Nabvala bafuta ndi guta woti biriwiri.

23. Mwamuna wace adziwika kubwalo,Pokhala pakati pa akuru a dziko.

24. Asoka maraya abafuta, nawagulitsa;Napereka mipango kwa wogulitsa malonda.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 31