Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 30:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Msundu uli ndi ana akazi awiri ati, Patsa, patsa,Pali zinthu zitatu sizikhuta konse,Ngakhale zinai sizinena, Kwatha:

16. Manda, ndi cumba,Dziko losakhuta madzi,Ndi moto wosanena, Kwatha.

17. Diso locitira atate wace ciphwete, ndi kunyoza kumvera amace,Makungubwi a kumtsinje adzalikolowola, ana a mphungu adzalidya,

Werengani mutu wathunthu Miyambi 30