Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 29:6-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. M'kulakwa kwa woipa muli msampha;Koma wolungama ayimba, nakondwera.

7. Wolungama asamalira mlandu wa osauka;Koma woipa alibe nzeru yakuudziwa.

8. Anthu onyoza atentha mudzi;Koma anzeru alezetsa mkwiyo.

9. Munthu wanzeru akatsutsana ndi munthu wopusa,Ngakhale akwiya, ngakhale aseka, palibe mtendere.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 29