Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 28:25-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Wodukidwa mtima aputa makangano;Koma wokhulupirira Yehova adzakula.

26. Wokhulupirira mtima wace wace ali wopusa;Koma woyenda mwanzeru adzapulumuka,

27. Wogawira aumphawi sadzasowa;Koma wophimba maso ace adzatembereredwa kwambiri.

28. Pouka oipa anthu amabisala;Koma pakufa amenewo olungama acuruka.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 28