Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 27:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Citsulo cinola citsulo;Comweco munthu anola nkhope ya mnzace.

18. Wosunga mkuyu adzadya zipatso zace;Wosamalira ambuyace adzalemekezedwa.

19. Monga m'madzi nkhope zionana,Momwemo mitima ya anthu idziwana.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 27