Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 27:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Usanyadire zamawa,Popeza sudziwa tsiku lina lidzabala ciani?

2. Wina akutame, si m'kamwamwako ai;Mlendo, si milomo ya iwe wekha.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 27