Monga cisanu ca cipale cofewa pa nthawi ya masika,Momwemo mthenga wokhulupirika kwa amene anamtuma;Atsitsimutsa moyo wa ambuyace.