Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 24:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukanena, Taonani, sitinadziwa cimeneci;Kodi woyesa mitima sacizindikira ici?Ndi wosunga moyo wako kodi sacidziwa?Ndipo kodi sabwezera munthu yense monga mwa macitidwe ace?

Werengani mutu wathunthu Miyambi 24

Onani Miyambi 24:12 nkhani