Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 23:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Udzammenya ndi ntyole,Nudzapulumutsa moyo wace kunsi kwa manda.

15. Mwananga, mtima wako ukakhala wanzeru,Mtima wanga wa inedi udzakondwa;

16. Imso zanga zidzasangalala,Polankhula milomo yako zoongoka.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 23