Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 23:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamene ukhala ulinkudya ndi mkuru,Zikumbukira ameneyo ali pamaso pako;

2. Nuike mpeni pakhosi pako,Ngati uli wadyera.

3. Usakhumbe zolongosoka zace;Pokhala zakudya zonyenga.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 23