Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 22:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri;Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi.

2. Wolemera ndi wosauka akumana,Wolenga onsewo ndiye Yehova.

3. Wocenjera aona zoipa, nabisala;Koma acibwana angopitirira, nalipitsidwa.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 22