Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 21:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Kukhala pa ngondya ya tsindwi kufunikaKuposa kukhala m'nyumba ndi mkazi wolongolola.

10. Wamphulupulu mtima wace umkhumba zoipa;Sakomera mtima mnzace.

11. Polangidwa wonyoza, wacibwana alandira nzeru,Naphunzira pakuyang'ana pa wanzeru.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 21