Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 21:24-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Wonyada wodzikuza dzina lace ndiye wonyoza;Acita mwaukali modzitama.

25. Cifuniro ca wolesi cimupha;Cifukwa manja ace akana kugwira nchito.

26. Ena asirira modukidwa tsiku lonse;Koma wolungama amapatsa osamana.

27. Nsembe ya oipa inyansa;Makamaka pakudza nayo iwo mwaciwembu.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 21