Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 20:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Mfumu yokhala pa mpando waweruziraIpitikitsa zoipa zonse ndi maso ace.

9. Ndani anganene, Ndasambitsa mtima wanga,Ndayera opanda cimo?

10. Miyeso yosiyana, ndi malicero osiyana,Zonse ziwirizi zinyansa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 20