Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 20:28-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Cifundo ndi ntheradi zisunga mfumu;Cifundo cicirikiza mpando wace.

29. Ulemerero wa anyamata ndiwo mphamvu yao;Kukongola kwa nkhalamba ndi

30. Mikwingwirima yopweteka icotsa zoipa;Ndi mikwapulo ilowa m'kati mwa mimba.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 20