Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 20:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Usakonde tulo ungasauke;Phenyula maso, udzakhuta zakudya.

14. Wogula ati, Cacabe cimeneco.Koma atacoka adzitama.

15. Alipo golidi ndi ngale zambiri;Koma milomo yodziwa ndiyo cokometsera ca mtengo wapatari.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 20