Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 19:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Ukangofuna, mwananga, kusocera kusiya mau akudziwitsa,Leka kumva mwambo.

28. Mboni yopanda pace inyoza ciweruzo;M'kamwa mwa amphulupulu mumeza zoipa,

29. Akonzera onyoza ciweruzo,Ndi mikwingwirima pamsana pa opusa.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 19