Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 19:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wosauka woyenda mwangwiroAposa wokhetsa milomo ndi wopusa.

2. Kukhumba kosadziwa sikuli kwabwino;Ndipo wofulumira ndi mapazi ace amacimwa.

3. Utsiru wa munthu ukhotetsa njira yace;Mtima wace udandaula pa Yehova.

4. Cuma cionjezetsa mabwenzi ambiri;Koma mnzace wa waumphawi amleka.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 19