Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 19:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wosauka woyenda mwangwiroAposa wokhetsa milomo ndi wopusa.

2. Kukhumba kosadziwa sikuli kwabwino;Ndipo wofulumira ndi mapazi ace amacimwa.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 19