Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 17:25-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Mwana wopusa acititsa atate wace cisoni,Namvetsa zowawa amace wombala.

26. Kulipiritsa wolungama sikuli kwabwino,Ngakhale kukwapula akuru cifukwa aongoka mtima.

27. Wopanda cikamwakamwa apambana kudziwa;Ndipo wofatsa mtima ali wanzeru.

28. Ngakhalecitsirucikatontholaaciyesa canzeru;Posunama ali wocenjera.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 17