Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 17:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nyenyeswa youma, pokhala mtendere,Iposa nyumba yodzala nyama yansembe, pali makangano.

2. Kapolo wocitamwanzeruAdzalamulira mwana wocititsa manyazi,Nadzagawana nao abale colowa.

3. Siliva ali ndi mbiya yosungunulira, golidi ali ndi ng'anjo;Koma Yehova ayesa mitima.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 17