Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 16:30-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Wotsinzina ndiye aganizira zakhota;Wosunama afikitsa zoipa.

31. Imvi ndiyo korona wa ulemu,Idzapezedwa m'njira ya cilungamo.

32. Wosakwiya msanga aposa wamphamvu;Wolamulira mtima wace naposa wolanda mudzi.

33. Maere aponyedwa pamfunga;Koma ndiye Yehova alongosola zonse.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 16