Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo adzadza kwa iwe, kucokera ku Asuri ndi midzi ya ku Aigupto, kuyambira ku Aigupto kufikira ku Mtsinje, ndi kuyambira kunyanja kufikira kunyanja, ndi kuyambira kuphiri kufikira kuphiri.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:12 nkhani