Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 6:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tamvani, mapiri inu, citsutsano ca Yehova, ndi inu maziko olimba a dziko lapansi; pakuti Yehova ali naco citsutsano ndi anthu ace, ndipo adzatsutsana ndi Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Mika 6

Onani Mika 6:2 nkhani