Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imva zowawa, nuyesetse kubala, mwana wamkazi wa Ziyoni, ngati mkazi wakubala; pakuti udzaturuka m'mudzi tsopano, nudzakhala kuthengo, nudzafika ku Babulo; komweko udzapulumutsidwa; komweko Yehova adzakuombola m'manja a adani ako.

Werengani mutu wathunthu Mika 4

Onani Mika 4:10 nkhani