Tamvanitu ici, akuru a nyumba ya Yakobo inu, ndi oweruza a nyumba ya Israyeli inu, akuipidwa naco ciweruzo, ndi kupotoza zoongoka zonse.