inu amene mukudyanso mnofu wa anthu anga; ndi kusenda khungu lao ndi kutyola mafupa ao; inde awaduladula ngati nyama yoti aphike, ndi ngati nyama ya mumphika.