Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 97:10-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Inuokonda Yehova, danani naco coipa:Iye asunga moyo wa okondedwa ace;Awalanditsa m'manja mwa oipa.

11. Kuunika kufesekera wolungama, Ndi cikondwerero oongoka mtima.

12. Kondwerani mwa Yehova, olungama inu;Ndipo yamikani pokumbukila ciyero cace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 97