Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 95:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Pamene makolo anu anandisuntha,Anandiyesa, anapenyanso cocita Ine.

10. Zaka makumi anai mbadwo uwu unandimvetsa cisoni,Ndipo ndinati, Iwo ndiwo anthu osokerera mtima,Ndipo sadziwa njira zanga.

11. Cifukwa cace ndinalumbira mu mkwiyo wanga,Ngati adzalowa mpumulo wanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 95