Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 95:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Pakuti Yehova ndiye Mulungu wamkuru;Ndi mfumu yaikuru yoposa milungu yonse.

4. Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lace;Cuma ca m'mapiri comwe ndi cace.

5. Nyanja ndi yace, anailenga;Ndipo manja ace anaumba dziko louma.

6. Tiyeni, tipembedze tiwerame;Tigwade pamaso pa Yehova, amene anatilenga:

Werengani mutu wathunthu Masalmo 95