Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 89:37-39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

37. Udzakhazikika ngati mwezi ku nthawi yonse,Ndi ngati mboni yokhulupirika kuthambo.

38. Koma Inu munamtaya, nimunamkaniza,Munakwiya naye wodzozedwa wanu.

39. Munakaniza cipangano ca mtumiki wanu;Munaipsa korona wace ndi kumponya pansi,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 89