Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 89:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndinacita cipangano ndi wosankhika wanga,Ndinalumbirira Davide mtumiki wanga:

4. Ndidzakhazika mbeu yako ku nthawi yonse,Ndipo ndidzamanga mpando wacifumu wako ku mibadwo mibadwo.

5. Ndipo kumwamba kudzalemekeza zodabwiza zanu, Yehova;Cikhulupiriko canunso mu msonkhano wa oyera mtima.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 89