Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 87:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Ndipo adzanena za Ziyoni,Uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo;Ndipo Wam'mwambamwamba ndiye aclzaukhazikitsa.

6. Yehova adzawerenga, polembera mitundu ya anthu.Uyu anabadwa komweko.

7. Ndipo oyimba ndi oomba omwe adzati,Akasupe ansa onse ali mwa inu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 87