Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 86:16-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Mundibwerere ine, ndi kundicitira cifundo;Mpatseni mtumiki wanu mphamvu yanu,Ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.

17. Mundicitire cizindikilo coti cabwino;Kuti ondida acione, nacite manyazi,Popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 86