Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 86:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe;Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi.

2. Sungani moyo wanga pakuti ine ndine wokondedwa wanu;Inu Mulungu wanga, pulumutsani mtumiki wanu wokhulupirira Inu.

3. Mundicitire cifundo, Ambuye;Pakuti tsiku lonse ndiitana Inu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 86