Ndidzamva colankhula Mulungu Yehova;Pakuti adzalankhula zamtendere ndi anthu ace, ndi okondedwa ace;Koma asabwererenso kucita zapusa.