Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 85:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Munacita zobvomereza dziko lanu, Yehova;Munabweza ukapolo wa Yakobo.

2. Munacotsa mphulupulu ya anthu anu,Munafotsera zolakwa zao zonse.

3. Munabweza kuzaza kwanu konse;Munabwerera ku mkwiyo wanu wotentha.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 85