Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 84:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pokhala Inu mpotikonda ndithu, Yehova wa makamu!

2. Moyo wanga ulakalaka, inde ukomokanso ndi kufuna mabwalo a Yehova;Mtima wanga ndi thupi langa zipfuulira kwa Mulungu wamoyo.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 84