Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 82:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Pulumutsani osauka ndi aumphawi:Alanditseni m'dzanja la oipa,

5. Sadziwa, ndipo sazindikira;Amayendayenda mumdima;Maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.

6. Ndinati Ine, Inu ndinu milungu,Ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 82