Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 81:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yimbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu;Pfuulirani kwa Mulungu wa Yakobo.

2. Utsani Salimo, bwera nakoni kalingaka,Zeze wokondwetsa pamodzi ndi cisakasa.

3. Ombani lipenga, pokhala mwezi,Utakula mwezi, tsiku la phwando lathu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 81